2 Mafumu 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Aava+ anapanga Nibazi ndi Tarataka, pamene Asefaravaimu+ anali kuwotcha ana awo aamuna pamoto+ powapereka nsembe kwa Adarameleki ndi Anameleki, milungu ya Sefaravaimu. Yesaya 37:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu,+ Hena, ndi Iva?’”+
31 Aava+ anapanga Nibazi ndi Tarataka, pamene Asefaravaimu+ anali kuwotcha ana awo aamuna pamoto+ powapereka nsembe kwa Adarameleki ndi Anameleki, milungu ya Sefaravaimu.
13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu,+ Hena, ndi Iva?’”+