2 Samueli 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Toi, mfumu ya Hamati+ anamva kuti Davide wapha gulu lonse lankhondo la Hadadezeri.+ Yesaya 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi milungu ya Hamati+ ndi Aripadi+ ili kuti? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu?+ Kodi yalanditsa Samariya m’manja mwanga?+
19 Kodi milungu ya Hamati+ ndi Aripadi+ ili kuti? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu?+ Kodi yalanditsa Samariya m’manja mwanga?+