Yeremiya 49:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+
23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+