2 Samueli 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Toi, mfumu ya Hamati+ anamva kuti Davide wapha gulu lonse lankhondo la Hadadezeri.+ 2 Mafumu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu, Hena, ndi Iva?’”+
13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu, Hena, ndi Iva?’”+