2 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+ 1 Mbiri 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo Davide anauza mwana wake Solomo kuti: “Ineyo, ndinafunitsitsa ndi mtima wanga wonse+ kumanga nyumba ya dzina+ la Yehova Mulungu wanga. Salimo 132:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+
2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+
7 Ndipo Davide anauza mwana wake Solomo kuti: “Ineyo, ndinafunitsitsa ndi mtima wanga wonse+ kumanga nyumba ya dzina+ la Yehova Mulungu wanga.
5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+