-
2 Samueli 6:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pamapeto pake uthenga unafika kwa Mfumu Davide wonena kuti: “Yehova wadalitsa nyumba ya Obedi-edomu ndi zake zonse chifukwa cha likasa la Mulungu woona.” Davide atamva mawu amenewa anapita kukatenga likasa la Mulungu woona kunyumba kwa Obedi-edomu ndi kupita nalo ku Mzinda wa Davide, akusangalala.+
-