1 Mbiri 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Davide+ ndi akulu a Isiraeli+ ndiponso atsogoleri+a anthu 1,000 aliyense, anali kuyenda mosangalala+ kupita kunyumba kwa Obedi-edomu,+ kukatenga likasa la pangano la Yehova. Salimo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Tukulani mitu yanu, inu zipata,+Ndipo dzitukuleni, inu makomo akale lomwe,+Kuti Mfumu yaulemerero ilowe!”+ Salimo 68:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo aona magulu anu a anthu opambana akuyendera pamodzi, inu Mulungu,+Magulu a anthu oyendera pamodzi a Mulungu wanga, Mfumu yanga, akukalowa kumalo oyera.+
25 Koma Davide+ ndi akulu a Isiraeli+ ndiponso atsogoleri+a anthu 1,000 aliyense, anali kuyenda mosangalala+ kupita kunyumba kwa Obedi-edomu,+ kukatenga likasa la pangano la Yehova.
7 “Tukulani mitu yanu, inu zipata,+Ndipo dzitukuleni, inu makomo akale lomwe,+Kuti Mfumu yaulemerero ilowe!”+
24 Iwo aona magulu anu a anthu opambana akuyendera pamodzi, inu Mulungu,+Magulu a anthu oyendera pamodzi a Mulungu wanga, Mfumu yanga, akukalowa kumalo oyera.+