14 Koma Mose anakwiya nawo kwambiri atsogoleri a nkhondowo,+ atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100, amene anachokera kunkhondo.
12 Idzaika anthu ena kukhala atsogoleri a magulu a anthu 1,000+ ndi atsogoleri a magulu a anthu 50.+ Ena azidzalima minda yake+ ndi kukolola mbewu zake,+ ndiponso ena azidzapanga zida zake zankhondo+ ndi zida zogwiritsa ntchito pamagaleta ake.+