-
Numeri 31:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma Mose anakwiya kwambiri ndi amuna amene ankatsogolera asilikaliwo, atsogoleri a magulu a asilikali 1,000 ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100, amene ankachokera kunkhondo.
-