Numeri 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mose anakwiya nawo kwambiri atsogoleri a nkhondowo,+ atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100, amene anachokera kunkhondo.
14 Koma Mose anakwiya nawo kwambiri atsogoleri a nkhondowo,+ atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100, amene anachokera kunkhondo.