2 Samueli 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide ndi nyumba yonse ya Isiraeli anali kupita ndi likasa+ la Yehova, akufuula mokondwera+ ndi kuimba lipenga la nyanga ya nkhosa.+ Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Salimo 97:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kwalengeza za chilungamo chake,+Ndipo mitundu yonse ya anthu yaona ulemerero wake.+
15 Davide ndi nyumba yonse ya Isiraeli anali kupita ndi likasa+ la Yehova, akufuula mokondwera+ ndi kuimba lipenga la nyanga ya nkhosa.+
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+