2 Mbiri 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho analumbira+ kwa Yehova ndi mawu okweza ndi kufuula mwachimwemwe, ndi kuliza malipenga ndi nyanga. Salimo 150:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+
14 Choncho analumbira+ kwa Yehova ndi mawu okweza ndi kufuula mwachimwemwe, ndi kuliza malipenga ndi nyanga.
3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+