1 Mbiri 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aisiraeli onse anali kupita ndi likasa la pangano la Yehova akufuula mokondwera,+ ndiponso akuliza nyanga za nkhosa+ ndi malipenga.+ Iwo anali kuimbanso mokweza zinganga,+ zoimbira za zingwe, ndi azeze.+ Salimo 81:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa tsiku lokhala mwezi, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+Pa tsiku looneka mwezi wathunthu, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, loimba pa tsiku la chikondwerero.+ Salimo 98:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Fuulani mwa kuimba malipenga ndi mphalasa.*+Fuulani mosangalala pamaso pa Mfumu Yehova, chifukwa wapambana.
28 Aisiraeli onse anali kupita ndi likasa la pangano la Yehova akufuula mokondwera,+ ndiponso akuliza nyanga za nkhosa+ ndi malipenga.+ Iwo anali kuimbanso mokweza zinganga,+ zoimbira za zingwe, ndi azeze.+
3 Pa tsiku lokhala mwezi, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+Pa tsiku looneka mwezi wathunthu, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, loimba pa tsiku la chikondwerero.+
6 Fuulani mwa kuimba malipenga ndi mphalasa.*+Fuulani mosangalala pamaso pa Mfumu Yehova, chifukwa wapambana.