2 Samueli 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide ndi nyumba yonse ya Isiraeli anali kupita ndi likasa+ la Yehova, akufuula mokondwera+ ndi kuimba lipenga la nyanga ya nkhosa.+ 1 Mbiri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+
15 Davide ndi nyumba yonse ya Isiraeli anali kupita ndi likasa+ la Yehova, akufuula mokondwera+ ndi kuimba lipenga la nyanga ya nkhosa.+
8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+