Ekisodo 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano Bezaleli+ anapanga Likasa+ la mtengo wa mthethe, mikono iwiri ndi hafu m’litali, mkono umodzi ndi hafu m’lifupi, ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+ Salimo 132:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani, inu Yehova, kuti mulowe kumalo anu okhalamo,+Inu pamodzi ndi Likasa+ limene mumasonyezera mphamvu zanu.+
37 Tsopano Bezaleli+ anapanga Likasa+ la mtengo wa mthethe, mikono iwiri ndi hafu m’litali, mkono umodzi ndi hafu m’lifupi, ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+
8 Nyamukani, inu Yehova, kuti mulowe kumalo anu okhalamo,+Inu pamodzi ndi Likasa+ limene mumasonyezera mphamvu zanu.+