Ekisodo 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Bezaleli+ anapanga Likasa+ la mtengo wa mthethe masentimita 110* mulitali, masentimita 70 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi kupita mʼmwamba.+
37 Kenako Bezaleli+ anapanga Likasa+ la mtengo wa mthethe masentimita 110* mulitali, masentimita 70 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi kupita mʼmwamba.+