Ekisodo 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkati mwake udzaikemo likasa la Umboni+ ndipo udzatchinge kumene kuli Likasalo ndi katani.+ Numeri 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho iwo ananyamuka kuphiri la Yehova,+ nʼkuyenda ulendo wa masiku atatu. Likasa+ la pangano la Yehova linali patsogolo pawo ulendo wa masiku atatu wonsewo, mpaka atapeza malo oti amangepo msasa.+
33 Choncho iwo ananyamuka kuphiri la Yehova,+ nʼkuyenda ulendo wa masiku atatu. Likasa+ la pangano la Yehova linali patsogolo pawo ulendo wa masiku atatu wonsewo, mpaka atapeza malo oti amangepo msasa.+