Numeri 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mukamasamutsa msasa, Aroni ndi ana ake azilowa mʼchihema nʼkuchotsa katani+ ndipo aziphimba likasa+ la Umboni ndi kataniyo. Aheberi 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+
5 Mukamasamutsa msasa, Aroni ndi ana ake azilowa mʼchihema nʼkuchotsa katani+ ndipo aziphimba likasa+ la Umboni ndi kataniyo.
3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+