Ekisodo 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkati mwake, udzaikemo likasa la umboni+ ndi kutchinga kumene kuli Likasalo ndi nsalu.+