Ekisodo 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkati mwake udzaikemo likasa la Umboni+ ndipo udzatchinge kumene kuli Likasalo ndi katani.+