Ekisodo 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mupange likasa* la mtengo wa mthethe, masentimita 110* mulitali, masentimita 70 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi kupita mʼmwamba.+ Ekisodo 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzapange chivundikiro chagolide woyenga bwino, masentimita 110 mulitali ndi masentimita 70 mulifupi.+
10 Mupange likasa* la mtengo wa mthethe, masentimita 110* mulitali, masentimita 70 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi kupita mʼmwamba.+
17 Mudzapange chivundikiro chagolide woyenga bwino, masentimita 110 mulitali ndi masentimita 70 mulifupi.+