Ekisodo 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Inetu ndikuitana ndi kutchula dzina Bezaleli+ mwana wamwamuna wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda.+ Ekisodo 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Bezaleli+ mwana wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda, anachita zonse zimene Yehova analamula Mose.
2 “Inetu ndikuitana ndi kutchula dzina Bezaleli+ mwana wamwamuna wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda.+
22 Bezaleli+ mwana wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda, anachita zonse zimene Yehova analamula Mose.