Ekisodo 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Mose anauza ana a Isiraeli kuti: “Yehova waitana ndi kutchula dzina Bezaleli,+ mwana wamwamuna wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda. 1 Mbiri 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Hura anabereka Uri.+ Uri anabereka Bezaleli.+
30 Kenako Mose anauza ana a Isiraeli kuti: “Yehova waitana ndi kutchula dzina Bezaleli,+ mwana wamwamuna wa Uri, mwana wa Hura wa fuko la Yuda.