37Tsopano Bezaleli+ anapanga Likasa+ la mtengo wa mthethe, mikono iwiri ndi hafu m’litali, mkono umodzi ndi hafu m’lifupi, ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+
5 Ndipo guwa lansembe lamkuwa+ limene Bezaleli+ mwana wa Uri mwana wa Hura+ anapanga, anali ataliika patsogolo pa chihema chopatulika cha Yehova. Choncho Solomo ndi mpingowo anafunsira paguwalo monga mwa nthawi zonse.