Ekisodo 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano Bezaleli+ anapanga Likasa+ la mtengo wa mthethe, mikono iwiri ndi hafu m’litali, mkono umodzi ndi hafu m’lifupi, ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+
37 Tsopano Bezaleli+ anapanga Likasa+ la mtengo wa mthethe, mikono iwiri ndi hafu m’litali, mkono umodzi ndi hafu m’lifupi, ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+