1 Mafumu 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mulungu anapitiriza kupatsa Solomo nzeru zopanda malire ndi luso lomvetsa zinthu losaneneka.+ Anam’patsanso mtima wozindikira zinthu mwakuya.+ Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+ 2 Petulo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuwonjezera apo, muone kuleza mtima kwa Ambuye wathu kukhala chipulumutso, monganso mmene m’bale wathu wokondedwa Paulo anakulemberani mogwirizana ndi nzeru+ zimene anapatsidwa.+
29 Mulungu anapitiriza kupatsa Solomo nzeru zopanda malire ndi luso lomvetsa zinthu losaneneka.+ Anam’patsanso mtima wozindikira zinthu mwakuya.+
15 Kuwonjezera apo, muone kuleza mtima kwa Ambuye wathu kukhala chipulumutso, monganso mmene m’bale wathu wokondedwa Paulo anakulemberani mogwirizana ndi nzeru+ zimene anapatsidwa.+