Salimo 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munsanja zokhalamo za m’mudzimo, Mulungu wadziwika kuti ndi malo okwezeka ndiponso achitetezo.+ Salimo 125:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wazungulira anthu ake+Ngati mmene mapiri azungulirira Yerusalemu,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+
2 Yehova wazungulira anthu ake+Ngati mmene mapiri azungulirira Yerusalemu,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+