-
Salimo 50:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pereka nsembe zoyamikira kwa Mulungu,+
Ndipo pereka kwa Wam’mwambamwamba zimene walonjeza.+
-
Salimo 66:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndidzalowa m’nyumba yanu ndi nsembe zopsereza zathunthu.+
Ine ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa inu+
-
-
-