Salimo 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa cha zimene mwachita ndidzakutamandani mumpingo waukulu.+Ndidzakwaniritsa malonjezo anga pamaso pa anthu oopa iye.+ Salimo 76:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu nonse amene mwazungulira Mulungu, lonjezani ndi kukwaniritsa malonjezo anuwo kwa Yehova Mulungu wanu.+Bweretsani mphatso mwamantha.+ Mlaliki 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuli bwino kuti usalonjeze+ kusiyana ndi kulonjeza koma osakwaniritsa zimene walonjezazo.+
25 Chifukwa cha zimene mwachita ndidzakutamandani mumpingo waukulu.+Ndidzakwaniritsa malonjezo anga pamaso pa anthu oopa iye.+
11 Inu nonse amene mwazungulira Mulungu, lonjezani ndi kukwaniritsa malonjezo anuwo kwa Yehova Mulungu wanu.+Bweretsani mphatso mwamantha.+