2 Mbiri 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pambuyo pa zimenezi, panali anthu ambiri amene ankabweretsa mphatso+ kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwinozabwino kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye anakwezeka+ m’maso mwa mitundu yonse. Salimo 68:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha kachisi wanu yemwe ali ku Yerusalemu,+Mafumu adzabweretsa mphatso kwa inu.+ Salimo 89:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+
23 Pambuyo pa zimenezi, panali anthu ambiri amene ankabweretsa mphatso+ kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwinozabwino kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye anakwezeka+ m’maso mwa mitundu yonse.
7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+