Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako mfumukaziyo inapatsa+ mfumuyo golide wokwana matalente* 120,+ mafuta a basamu+ ochuluka zedi, ndi miyala yamtengo wapatali. Mafuta a basamu amene mfumukazi ya ku Sheba inapatsa Mfumu Solomo, anali ochuluka kwambiri moti sipanakhalenso mafuta ochuluka ngati amenewo.

  • 2 Mbiri 32:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pambuyo pa zimenezi, panali anthu ambiri amene ankabweretsa mphatso+ kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwinozabwino kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye anakwezeka+ m’maso mwa mitundu yonse.

  • Salimo 72:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+

      Adzapereka msonkho.+

      Mafumu a ku Sheba ndi Seba

      Adzapereka mphatso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena