Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Nyale ya Mulungu inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona m’kachisi+ wa Yehova, mmene munali likasa la Mulungu.

  • 1 Mafumu 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova.+ Anayamba kuchita zimenezi m’chaka cha 480 kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo,+ m’mwezi wachiwiri+ wa Zivi.+ Ichi chinali chaka chachinayi+ cha ulamuliro wake monga mfumu ya Isiraeli.

  • 1 Mbiri 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+

  • Ezara 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Komanso, ziwiya zagolide ndi zasiliva+ zimene Nebukadinezara anazitenga m’kachisi wa Mulungu yemwe anali ku Yerusalemu, n’kupita nazo kukachisi wa ku Babulo,+ mfumu Koresi+ inazichotsa m’kachisi wa ku Babuloyo. Ndiyeno zinaperekedwa kwa Sezibazara,+ munthu amene Koresi anamuika kukhala bwanamkubwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena