Numeri 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose m’chipululu cha Sinai,+ m’chihema chokumanako.+ Analankhula naye pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri m’chaka chachiwiri, atatuluka m’dziko la Iguputo.+ Iye anati:
1 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose m’chipululu cha Sinai,+ m’chihema chokumanako.+ Analankhula naye pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri m’chaka chachiwiri, atatuluka m’dziko la Iguputo.+ Iye anati: