Ekisodo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 M’mwezi wachitatu kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo,+ pa tsiku lomwelo,* iwo analowa m’chipululu cha Sinai.+ Deuteronomo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+ Machitidwe 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu.
19 M’mwezi wachitatu kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo,+ pa tsiku lomwelo,* iwo analowa m’chipululu cha Sinai.+
2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+
38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu.