Yesaya 66:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+ Luka 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno Mariya anati: “Ndinetu kapolo wa Yehova!+ Zimene mwanenazo zichitike ndithu kwa ine.” Pamenepo mngeloyo anamusiya. Aheberi 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, tiyeni tiyandikire mpando wachifumu wa kukoma mtima kwakukulu ndipo tipemphere kwa Mulungu+ ndi ufulu wa kulankhula,+ kuti atichitire chifundo ndi kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi imene tikufunika thandizo.+
2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+
38 Ndiyeno Mariya anati: “Ndinetu kapolo wa Yehova!+ Zimene mwanenazo zichitike ndithu kwa ine.” Pamenepo mngeloyo anamusiya.
16 Choncho, tiyeni tiyandikire mpando wachifumu wa kukoma mtima kwakukulu ndipo tipemphere kwa Mulungu+ ndi ufulu wa kulankhula,+ kuti atichitire chifundo ndi kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi imene tikufunika thandizo.+