Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 30:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 mwamuna wake n’kumva koma osanena kanthu kwa iye pa tsiku limene wamva mawu a lonjezolo, malonjezo ake a kudzimana amene walumbirira moyo wake akhale momwemo.+

  • Numeri 30:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ngati mwamunayo sananenepo kanthu kwa mkazi wake, masiku n’kumapita, ndiye kuti mwamunayo wakhazikitsa malonjezo onse a mkaziyo, kapena malonjezo onse odzimana amene mkaziyo walumbirira moyo wake.+ Iye wawakhazikitsa chifukwa sananenepo kanthu kwa mkaziyo pa tsiku limene anamumva akulonjeza.

  • Deuteronomo 23:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Uzisunga mawu a pakamwa pako+ ndipo uzikwaniritsa lonjezo limene unapereka kwa Yehova Mulungu wako monga nsembe yaufulu. Uzichita zimenezi chifukwa unalonjeza ndi pakamwa pako.+

  • Mlaliki 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena