Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho Yezebeli analemba makalata+ m’dzina la Ahabu n’kuwadinda ndi chidindo cha Ahabu.+ Kenako anatumiza makalatawo kwa akulu+ ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzinda umodzi ndi Naboti.

  • 2 Mbiri 32:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 lye analembanso makalata+ onyoza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ komanso omutonza kuti: “Mofanana ndi milungu+ ya mitundu ya mayiko ena imene sinapulumutse anthu ake m’manja mwanga,+ Mulungu wa Hezekiya sapulumutsa anthu ake m’manja mwanga.”

  • Nehemiya 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako Sanibalati+ ananditumizira uthenga wofananawo ulendo wachisanu kudzera mwa mtumiki wake. Mtumikiyo anali ndi kalata yosatseka m’manja mwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena