2 Mafumu 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Hezekiya anatenga kalatayo m’manja mwa amithengawo n’kuiwerenga.+ Pambuyo pake iye anapita nayo kunyumba ya Yehova n’kukaitambasula pamaso pa Yehova.+ Nehemiya 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Sanibalati+ ananditumizira uthenga wofananawo ulendo wachisanu kudzera mwa mtumiki wake. Mtumikiyo anali ndi kalata yosatseka m’manja mwake.
14 Kenako Hezekiya anatenga kalatayo m’manja mwa amithengawo n’kuiwerenga.+ Pambuyo pake iye anapita nayo kunyumba ya Yehova n’kukaitambasula pamaso pa Yehova.+
5 Kenako Sanibalati+ ananditumizira uthenga wofananawo ulendo wachisanu kudzera mwa mtumiki wake. Mtumikiyo anali ndi kalata yosatseka m’manja mwake.