Yesaya 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Hezekiya anatenga kalatayo m’manja mwa amithengawo n’kuiwerenga.+ Pambuyo pake iye anapita nayo kunyumba ya Yehova, n’kuitambasula pamaso pa Yehova.+
14 Kenako Hezekiya anatenga kalatayo m’manja mwa amithengawo n’kuiwerenga.+ Pambuyo pake iye anapita nayo kunyumba ya Yehova, n’kuitambasula pamaso pa Yehova.+