2 Mafumu 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi milungu+ ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawalanditsa? Kodi inalanditsa Gozani,+ Harana,+ Rezefi ndi ana a Edeni+ amene anali ku Tela-sara?+
12 Kodi milungu+ ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawalanditsa? Kodi inalanditsa Gozani,+ Harana,+ Rezefi ndi ana a Edeni+ amene anali ku Tela-sara?+