Deuteronomo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno munafika pamalo ano, ndipo Sihoni mfumu ya Hesiboni+ ndi Ogi+ mfumu ya Basana anatuluka kudzamenyana nafe nkhondo, koma tinawagonjetsa.+ Yoswa 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tamvanso zonse zimene anachita kwa mafumu awiri a Aamori kutsidya lina la Yorodano. Mafumuwo ndiwo Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali ku Asitaroti.+
7 Ndiyeno munafika pamalo ano, ndipo Sihoni mfumu ya Hesiboni+ ndi Ogi+ mfumu ya Basana anatuluka kudzamenyana nafe nkhondo, koma tinawagonjetsa.+
10 Tamvanso zonse zimene anachita kwa mafumu awiri a Aamori kutsidya lina la Yorodano. Mafumuwo ndiwo Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali ku Asitaroti.+