Deuteronomo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Apa n’kuti atagonjetsa Sihoni+ mfumu ya Aamori imene inali kukhala ku Hesiboni. Anali atagonjetsanso Ogi+ mfumu ya Basana imene inali kukhala ku Asitaroti.+ Mfumu imeneyi anaigonjetsera ku Edirei.+ Yoswa 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumu ina ndi Ogi+ wa ku Basana yemwe anali mmodzi mwa Arefai+ otsala, ndipo ankakhala ku Asitaroti+ ndi ku Edirei.+
4 Apa n’kuti atagonjetsa Sihoni+ mfumu ya Aamori imene inali kukhala ku Hesiboni. Anali atagonjetsanso Ogi+ mfumu ya Basana imene inali kukhala ku Asitaroti.+ Mfumu imeneyi anaigonjetsera ku Edirei.+
4 Mfumu ina ndi Ogi+ wa ku Basana yemwe anali mmodzi mwa Arefai+ otsala, ndipo ankakhala ku Asitaroti+ ndi ku Edirei.+