Deuteronomo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Apa nʼkuti atagonjetsa Sihoni+ mfumu ya Aamori imene inkakhala ku Hesiboni komanso Ogi+ mfumu ya Basana imene inkakhala ku Asitaroti. Mfumu imeneyi anaigonjetsera ku Edirei.+
4 Apa nʼkuti atagonjetsa Sihoni+ mfumu ya Aamori imene inkakhala ku Hesiboni komanso Ogi+ mfumu ya Basana imene inkakhala ku Asitaroti. Mfumu imeneyi anaigonjetsera ku Edirei.+