Yoswa 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa fuko la Rubeni ndi kwa fuko la Gadi, kutsidya lakumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano.+ Yoswa 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafukowa anapatsidwanso dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi mfumu ya Basana, imene inali kulamulira ku Asitaroti ndi ku Edirei. (Mfumu Ogi inali mmodzi mwa Arefai otsala.)+ Mose anagonjetsa anthu onsewa nʼkuwathamangitsa.+
8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa fuko la Rubeni ndi kwa fuko la Gadi, kutsidya lakumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano.+
12 Mafukowa anapatsidwanso dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi mfumu ya Basana, imene inali kulamulira ku Asitaroti ndi ku Edirei. (Mfumu Ogi inali mmodzi mwa Arefai otsala.)+ Mose anagonjetsa anthu onsewa nʼkuwathamangitsa.+