33 Pambuyo pake, anatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana.+ Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kukamenyana nawo pankhondo ya ku Edirei.+
3“Ndiyeno tinatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana. Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kudzamenyana nafe nkhondo ku Edirei.+