Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Apa n’kuti atagonjetsa Sihoni+ mfumu ya Aamori imene inali kukhala ku Hesiboni. Anali atagonjetsanso Ogi+ mfumu ya Basana imene inali kukhala ku Asitaroti.+ Mfumu imeneyi anaigonjetsera ku Edirei.+

  • Deuteronomo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mwa Arefai+ onse, Ogi yekha mfumu ya Basana ndi amene anali atatsala. Chithatha chimene anaikapo mtembo wake chinali chachitsulo. Kodi si chija chili ku Raba+ wa ana a Aamoni? N’chachitali mikono* 9, ndipo m’lifupi mwake mikono inayi, kutsatira muyezo wodziwika.

  • Deuteronomo 4:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 ndipo anamulanda dziko lakelo ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana. Amenewa ndi mafumu awiri a Aamori amene anali kuchigawo chotulukira dzuwa cha Yorodano.

  • Yoswa 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tamvanso zonse zimene anachita kwa mafumu awiri a Aamori kutsidya lina la Yorodano. Mafumuwo ndiwo Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali ku Asitaroti.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena