Numeri 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pambuyo pake, anatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana.+ Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kukamenyana nawo pankhondo ya ku Edirei.+ Numeri 21:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho Aisiraeliwo anapha iyeyo, ana ake ndi anthu ake onse, moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka,+ ndipo analanda dziko lake.+ Deuteronomo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Yehova Mulungu wathu anaperekanso Ogi mfumu ya Basana ndi anthu ake onse m’manja mwathu, ndipo tinam’kantha moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka mwa anthu ake.+
33 Pambuyo pake, anatembenuka ndi kulowera njira ya ku Basana.+ Pamenepo, Ogi+ mfumu ya Basana inatuluka pamodzi ndi anthu ake onse kukamenyana nawo pankhondo ya ku Edirei.+
35 Choncho Aisiraeliwo anapha iyeyo, ana ake ndi anthu ake onse, moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka,+ ndipo analanda dziko lake.+
3 Pamenepo Yehova Mulungu wathu anaperekanso Ogi mfumu ya Basana ndi anthu ake onse m’manja mwathu, ndipo tinam’kantha moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka mwa anthu ake.+