Yoswa 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumu ina ndi Ogi+ wa ku Basana yemwe anali mmodzi mwa Arefai+ otsala, ndipo ankakhala ku Asitaroti+ ndi ku Edirei.+ Yoswa 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose mtumiki wa Yehova ndi ana a Isiraeli ndiwo anagonjetsa mafumuwa.+ Atatero, Mose mtumiki wa Yehova anapereka dzikoli kwa Arubeni,+ Agadi,+ ndi hafu ya fuko la Manase,+ kuti likhale lawo.
4 Mfumu ina ndi Ogi+ wa ku Basana yemwe anali mmodzi mwa Arefai+ otsala, ndipo ankakhala ku Asitaroti+ ndi ku Edirei.+
6 Mose mtumiki wa Yehova ndi ana a Isiraeli ndiwo anagonjetsa mafumuwa.+ Atatero, Mose mtumiki wa Yehova anapereka dzikoli kwa Arubeni,+ Agadi,+ ndi hafu ya fuko la Manase,+ kuti likhale lawo.