Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+ Numeri 21:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho Aisiraeliwo anapha iyeyo, ana ake ndi anthu ake onse, moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka,+ ndipo analanda dziko lake.+
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
35 Choncho Aisiraeliwo anapha iyeyo, ana ake ndi anthu ake onse, moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka,+ ndipo analanda dziko lake.+