Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Sihoni+ mfumu ya Aamori, yemwe ankakhala ku Hesiboni.+ Dera lomwe anali kulamulira linkayambira pakatikati pa chigwa cha Arinoni kuphatikizapo mzinda wa Aroweli,+ umene unali m’mphepete mwa mtsinje wa Arinoni,+ mpaka hafu ya Giliyadi kukalekezera kuchigwa cha Yaboki,+ kumalire ndi ana a Amoni.

  • Oweruza 11:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo Yehova Mulungu wa Aisiraeli anapereka Sihoni ndi anthu ake onse m’manja mwa Aisiraeli. Choncho anawagonjetsa ndi kutenga dziko lonse la Aamori okhala kumeneko.+

  • Salimo 135:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amene anachita zimenezi ndi amene anakantha mitundu yambiri+

      Ndi kupha mafumu amphamvu.+

  • Salimo 136:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iye anapha Sihoni mfumu ya Aamori:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Amosi 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Koma ine ndinawononga Aamori+ chifukwa cha anthu anga. Aamoriwo misinkhu yawo inali yofanana ndi mitengo ya mkungudza ndipo mphamvu zawo zinali zofanana ndi za mitengo ikuluikulu.+ Ndinawononga zipatso zawo m’mwamba ndiponso mizu yawo pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena